Miyambi 25:26-28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

26. Monga kasupe wopondedwa, ndi citsime cobvonongeka,Momwemo wolungama ngati akonjera woipa.

27. Kudya uci wambiri sikuli kwabwino;Comweco kufunafuna ulemu wako wako sikuli ulemu.

28. Wosalamulira mtima waceAkunga mudzi wopasuka wopanda linga,

Miyambi 25