Miyambi 25:16-19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

16. Wapeza uci kodi? Idyapo wokwanira,Kuti ungakukole, nusanze.

17. Phazi lako lilowe m'nyumba ya mnzako kamodzi kamodzi;Kuti angatope nawe ndi kukuda.

18. Wocitira mnzace umboni wonamaNdiye cibonga, ndi lupanga, ndi mubvi wakuthwa.

19. Kukhulupirira munthu wa ciwembu tsiku latsokaKunga dzino lotyoka ndi phazi loguluka.

Miyambi 25