Miyambi 22:6-9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

6. Phunzitsa mwana poyamba njira yace;Ndipo angakhale atakalamba sadzacokamo.

7. Wolemera alamulira osauka;Ndipo wokongola ndiye kapolo wa womkongoletsa.

8. Wofesa zosalungama adzakolola tsoka;Ndipo ntyole ya mkwiyo wace idzalephera.

9. Mwini diso lamataya adzadala;Pakuti apatsa osauka zakudya zace.

Miyambi 22