Miyambi 20:12-14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

12. Khutu lakumva, ndi diso lopenya,Yehova anapanga onse awiriwo.

13. Usakonde tulo ungasauke;Phenyula maso, udzakhuta zakudya.

14. Wogula ati, Cacabe cimeneco.Koma atacoka adzitama.

Miyambi 20