Miyambi 2:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Mwananga, ukalandira mau anga,Ndi kusunga malamulo anga;

2. Kucherera makutu ako kunzeru,Kulozetsa mtima wako kukuzindikira;

3. Ukaitananso luntha,Ndi kupfuulira kuti ukazindikire;

Miyambi 2