Miyambi 19:9-11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

9. Mboni yonama sidzapulumuka cilango;Wolankhula mabodza adzaonongeka.

10. Wopusa sayenera kukhala ndi zinthu zolongosoka;Nanga kapolo ayenera kulamulira akalonga kodi?

11. Kulingalira kwa munthu kucedwetsa mkwiyo;Ulemerero wace uli wakuti akhululukire colakwa.

Miyambi 19