Miyambi 18:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Wopanduka afunafuna niro cace,Nakangana ndi nzeru yonse yeniyeni.

2. Wopusa sakondwera ndi kuzindikira;Koma kungobvumbulutsa za m'mtima mwace.

3. Pakudza wamphulupulu padzanso kunyoza;Manyazi natsagana ndi citonzo.

Miyambi 18