Miyambi 17:9-11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

9. Wobisa colakwa afunitsa cikondano;Koma wobwereza-bwereza mau afetsa ubwenzi.

10. Cidzudzulo cilowa m'kati mwa wozindikira,Kopambana ndi kukwapula wopusa kwambiri.

11. Woipa amafuna kupanduka kokha;Koma adzamtumizira mthenga wankhanza.

Miyambi 17