Miyambi 15:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Lilime la anzeru linena bwino zomwe adziwa;Koma m'kamwa mwa opusa mutsanulira utsiru.

Miyambi 15

Miyambi 15:1-5