Miyambi 14:34-35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

34. Cilungamo cikuza mtundu wa anthu;Koma cimo licititsa pfuko manyazi.

35. Mfumu ikomera mtima kapolo wocita mwanzeru;Koma idzakwiyira wocititsa manyazi.

Miyambi 14