Miyambi 14:19-21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

19. Oipa amagwadira abwino,Ndi ocimwa pa makomo a olungama.

20. Waumphawi adedwa ndi anzace omwe;Koma akukonda wolemera acuruka.

21. Wonyoza anzace acimwa;Koma wocitira osauka cifundo adala.

Miyambi 14