Miyambi 13:5-7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

5. Wolungama ada mau onama;Koma woipa anyansa, nadzicititsa manyazi,

6. Cilungamo cicinjiriza woongoka m'njira;Koma udio ugwetsa wocimwa.

7. Alipo wodziyesa wolemera, koma alibe kanthu;Alipo wodziyesa wosauka, koma ali ndi cuma cambiri.

Miyambi 13