Miyambi 13:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Malamulo a wanzeru ndiwo kasupe wa moyo,Apatutsa ku misampha ya imfa.

Miyambi 13

Miyambi 13:13-21