Miyambi 13:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Mwana wanzeru amamvera mwambo wa atate;Koma wonyoza samvera cidzudzulo.

2. Munthu adzadya zabwino ndi zipatso za m'kamwa mwace;Koma moyo wa aciwembu udzadya ciwawa.

Miyambi 13