Miyambi 11:27-29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

27. Wopwaira ubwino afunitsa cikondwerero;Koma zoipa zidzamfikira wozilondola.

28. Wokhulupmra cuma cace adzagwa;Koma olungama adzaphuka ngati tsamba.

29. Wobvuta banja lace adzalowa m'zomsautsa;Wopusa adzatumikira wanzeru.

Miyambi 11