Mika 7:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Adzanyambita pfumbi ngati njoka; ngati zokwawa za padziko, adzanjenjemera poturuka m'ngaka mwao; adzafika kwa Yehova Mulungu wao ndi mantha, nadzaopa cifukwa ca iwe.

Mika 7

Mika 7:8-19