Mika 7:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mudyetse anthu anu ndi ndodo yanu, nkhosa za colowa canu zokhala pa zokha m'nkhalango pakati pa Karimeli, zidye m'Basana ndi m'Gileadi masiku a kale lomwe.

Mika 7

Mika 7:6-20