Mika 6:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anthu anga, kumbukilanitu cofunsira Balaki mfumu ya Moabu, ndi comuyankha Balamu mwana wa Beori, kuyambira ku Sitimu kufikira ku Giligala; kuti mudziwe zolungama za Yehova.

Mika 6

Mika 6:1-9