Mika 2:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace atero Yehova, Taonani, ndilingirira coipa pa banja ili, cimene simudzacotsako makosi anu, kapena kuyenda modzikuza inu; Pakuti nyengo iyi ndi yoipa.

Mika 2

Mika 2:1-7