Mika 1:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Imvani, mitundu ya anthu, inu nonse; tamvera, dziko lapansi, ndi zonse ziri m'mwemo; ndipo Ambuye Yehova akhale mboni yakutsutsa inu, Ambuye m'Kacisi wace wopatulika.

Mika 1

Mika 1:1-10