Mika 1:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Manga gareta ku kavalo waliwiro, wokhala m'Lakisi iwe, woyamba kucimwitsa mwana wamkazi wa Ziyoni ndi iye; pakuti zolakwa za Israyeli zinapezedwa mwa iwe.

Mika 1

Mika 1:6-16