Mateyu 9:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yesu anayendayenda m'mizinda yonse ndi m'midzi, namaphunzitsa m'masunagoge mwao, nalalikira uthenga wabwino wa Ufumuwo, naciritsa nthenda iri yonse ndi zofoka zonse.

Mateyu 9

Mateyu 9:27-38