Mateyu 9:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Yesu potembenuka ndi kuona iye anati, Limba mtima, mwana wamkaziwe, cikhulupiriro cako cakuciritsa. Ndipo mkaziyo anacira kuyambira nthawi yomweyo.

Mateyu 9

Mateyu 9:21-25