Mateyu 9:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo onani, anabwera naye kwa Iye munthu wamanjenje, wakugona pachika: ndipo Yesu pakuona cikhulupiriro cao, anati kwa wodwalayo, Limba mtima, mwana, macimo ako akhululukidwa.

Mateyu 9

Mateyu 9:1-5