Mateyu 9:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kapena samathira vinyo watsopano m'matumba akale; akatero, matumba aphulika, ndi vinyo atayika, ndi matumba aonongeka: koma athira vinyo watsopano m'matumba atsopano, ndi zonse ziwiri zisungika.

Mateyu 9

Mateyu 9:10-19