Mateyu 9:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pomwepo anadza kwa Iye ophunzira ace a Yohane, nati, Cifukwa ninji ife ndi Afarisi tisala kudya kawiri kawiri, koma ophunzira anu sasala?

Mateyu 9

Mateyu 9:6-15