Mateyu 9:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali pamene Iye analinkukhala pacakudya m'nyumba, onani, amisonkho ndi ocimwa ambiri anadza nakhala pansi pamodzi ndi Yesu ndi ophunzira ace.

Mateyu 9

Mateyu 9:1-14