Mateyu 8:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti inenso ndiri munthu wakumvera ulamuliro, ndiri nao asilikari akundimvera ine: ndipo ndinena kwa uyu, Muka, namuka; ndi kwa wina, Idza, nadza; ndi kwa kapolo wanga, Cita ici, nacita.

Mateyu 8

Mateyu 8:8-17