Mateyu 8:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati kwa iyo, Mukani. Ndipo inaturuka, nimuka, kukalowa m'nkhumbazo; ndipo onani, gulu lonse linathamangira kunsi kuphompho m'nyanjamo, ndipo linafa m'madzi.

Mateyu 8

Mateyu 8:29-34