Mateyu 8:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yesu ananena kwa iye, Ankhandwe ali nazo nkhwimba zao, ndi mbalame za m'mlengalenga zisa zao, koma Mwana wa munthu alibe potsamira mutu wace.

Mateyu 8

Mateyu 8:12-30