Mateyu 8:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yesu anati kwa kenturiyoyo, Pita, kukhale kwa iwe monga unakhulupirira. Ndipo anaciritsidwa mnyamatayo nthawi yomweyo.

Mateyu 8

Mateyu 8:4-15