Mateyu 8:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinena ndi inu, kuti ambiri a kum'mawa ndi a kumadzulo adzafika, nadzakhala pamodzi ndi Abrahamu, ndi Isake, ndi Yakobo, mu Ufumu wa Kumwamba;

Mateyu 8

Mateyu 8:4-15