Mateyu 7:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kapena udzati bwanji kwa mbale wako, Tandilola ndicotse kacitsotso m'diso lako; ndipo ona, mtandawo ulimo m'diso lakoli.

Mateyu 7

Mateyu 7:1-7