Mateyu 7:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo inagwa mvula, nidzala mitsinje, ndipo zinaomba mphepo, zinagunda pa nyumbayo; ndipo inagwa; ndi kugwa kwace kunali kwakukuru.

Mateyu 7

Mateyu 7:23-29