Mateyu 7:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo inagwa mvula, nidzala mitsinje, ndipo zinaomba mphepo, zinagunda pa nyumbayo; koma siinagwa; cifukwa inakhazikika pathanthwepo.

Mateyu 7

Mateyu 7:19-28