Mateyu 6:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo muderanji nkhawa ndi cobvala? Tapenyetsani maluwa a kuthengo, makulidwe ao; sagwiritsa nchito, kapena sapota:

Mateyu 6

Mateyu 6:23-34