Mateyu 6:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace ndinena kwa inu, Musadere nkhawa moyo wanu, cimene mudzadya ndi cimene mudzamwa; kapena thupi lanu, cimene mudzabvala. Kodi moyo suli woposa cakudya, ndi thupi loposa cobvala?

Mateyu 6

Mateyu 6:24-27