Mateyu 6:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ngati diso lako liri loipa, thupi lako lonse lidzakhala lodetsedwa. Cifukwa cace ngati kuwala kumene kuli mwa inu kuli mdima, mdimawo ndi waukuru ndithu!

Mateyu 6

Mateyu 6:19-27