Mateyu 6:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti usaonekere kwa anthu kuti ulikusala kudya, koma kwa Atate wako ali m'tseri: ndipo Atate wako wakuona m'tseri adzakubwezera iwe.

Mateyu 6

Mateyu 6:12-28