Mateyu 5:45 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kotero kuti mukakhale ana a Atate wanu wa Kumwamba; cifukwa Iye amakwezera dzuwa lace pa oipa ndi pa abwino, namabvumbitsira mvula pa olungama ndi pa osalungama.

Mateyu 5

Mateyu 5:43-48