Mateyu 5:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti indetu ndinena kwa inu, Kufikira litapitirira thambo ndi dziko, kalemba kakang'ono kamodzi kapena kansonga kace kamodzi sikadzaeokera kucilamulo, kufikira zitacitidwa zonse.

Mateyu 5

Mateyu 5:15-28