Mateyu 5:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kapena sayatsa nyali, ndi kuibvundikira m'mbiya, koma aiika iyo pa coikapo cace; ndipo iunikira onse: ali m'nyumbamo.

Mateyu 5

Mateyu 5:8-25