Mateyu 5:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Inu ndinu mcere wa dziko lapansi; koma mcerewo ngati uka: sukuluka, adzaukoleretsa ndi ciani? Pamenepo sungakwanirenso kanthu konse, koma kuti ukaponyedwe kunja, nupondedwe ndi anthu.

Mateyu 5

Mateyu 5:4-23