nanena naye, Ngati muli Mwana wa Mulungu, mudzigwetse nokha pansi: pakuti kwalembedwa, kuti,Adzauza angelo ace za iwe,Ndipo pa manja ao adzakunyamulaiwe,Ungagunde konse phazi lako pamwala.