Mateyu 4:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yesu anayendayenda m'Galileya monse, analikuphunzitsa m'masunagoge mwao, nalalikira uthenga wabwino wa Ufumu, naciritsa nthenda zonse ndi kudwala konse mwa anthu.

Mateyu 4

Mateyu 4:22-25