Mateyu 4:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo popitirirapo Iye anaona abale ena awiri, Yakobo mwana wa Zebedayo, ndi Yohane mbale wace, m'ngalawa, pamodzi ndi Zebedayo atate wao, analikusoka makoka ao; ndipo anaitana iwo.

Mateyu 4

Mateyu 4:16-25