Mateyu 3:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye pakuona ambiri a Afarisi ndi a Asaduki akudza ku ubatizo wace, anati kwa iwo, Obadwa a njoka inu, ndani anakulangizani kuthawa mkwiyo ulinkudza?

Mateyu 3

Mateyu 3:6-15