Mateyu 28:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi kuwaphunzitsa, asunge zinthu zonse zimene ndinakulamulirani inu; ndipo onani, Ine ndiri pamodzi ndi inu masiku onse, kufikira cimariziro ca nthawi ya pansi pano.

Mateyu 28

Mateyu 28:13-20