Mateyu 28:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo onani, panali cibvomezi cacikuru; pakuti mngelo wa Ambuye anatsika Kumwamba, nafika kukunkhuniza mwalawo, nakhala pamwamba pace.

Mateyu 28

Mateyu 28:1-11