Mateyu 27:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo cinakwaniridwa conenedwa ndi Yeremiya mneneri, ndi kuti,Ndipo iwo anatenga ndalamazo zasiliva makumi atatu,Mtengo wa uja wowerengedwa mtengo wace,Amene iwo a ana a Israyeli anawerenga mtengo wace;

Mateyu 27

Mateyu 27:8-12